1 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya anthu ake,+ popeza Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+ Yeremiya 31:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Yehova wanena kuti: “‘Ngati kumwamba kungayezedwe ndipo ngati maziko a dziko lapansi angafufuzidwe, ndiye kuti inenso ndingakane mbadwa zonse za Isiraeli chifukwa cha zonse zimene achita,’ akutero Yehova.”+
22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya anthu ake,+ popeza Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+
37 Yehova wanena kuti: “‘Ngati kumwamba kungayezedwe ndipo ngati maziko a dziko lapansi angafufuzidwe, ndiye kuti inenso ndingakane mbadwa zonse za Isiraeli chifukwa cha zonse zimene achita,’ akutero Yehova.”+