Aroma 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngakhale kuti ankadziwa Mulungu, iwo sanamulemekeze monga Mulungu komanso sanamuthokoze. Mʼmalomwake anayamba kuganiza zinthu zopanda nzeru ndipo mitima yawo yopusayo inachita mdima.+
21 Ngakhale kuti ankadziwa Mulungu, iwo sanamulemekeze monga Mulungu komanso sanamuthokoze. Mʼmalomwake anayamba kuganiza zinthu zopanda nzeru ndipo mitima yawo yopusayo inachita mdima.+