Aroma 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Komanso, Yesaya analengeza zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ambiri ngati mchenga wakunyanja, ochepa okha ndi amene adzapulumuke.+
27 Komanso, Yesaya analengeza zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ambiri ngati mchenga wakunyanja, ochepa okha ndi amene adzapulumuke.+