23 Ndiponso bwanji ngati anachita zimenezo kuti asonyeze kukula kwa ulemerero wake kwa anthu oyenera kuwachitira chifundo,+ omwe anawakonzeratu kuti alandire ulemerero, 24 ndipo anthu ake ndi ifeyo amene anatiitana osati kuchokera kwa Ayuda okha komanso ku mitundu ina?+