Salimo 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zikanakhala bwino chipulumutso cha Isiraeli chikanachokera ku Ziyoni.+ Yehova akadzabwezeretsa anthu ake amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.
7 Zikanakhala bwino chipulumutso cha Isiraeli chikanachokera ku Ziyoni.+ Yehova akadzabwezeretsa anthu ake amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.