1 Timoteyo 2:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimenezi ndi zabwino ndiponso zovomerezeka kwa Mulungu, yemwe ndi Mpulumutsi wathu,+ 4 amene amafuna kuti anthu osiyanasiyana apulumuke+ nʼkukhala odziwa choonadi molondola.
3 Zimenezi ndi zabwino ndiponso zovomerezeka kwa Mulungu, yemwe ndi Mpulumutsi wathu,+ 4 amene amafuna kuti anthu osiyanasiyana apulumuke+ nʼkukhala odziwa choonadi molondola.