1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+ 3 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ndi udindo wathu kuwalandira bwino anthu amenewa+ komanso kuwachereza, kuti akhale antchito anzathu polengeza choonadi.+
8 Choncho, ndi udindo wathu kuwalandira bwino anthu amenewa+ komanso kuwachereza, kuti akhale antchito anzathu polengeza choonadi.+