-
Yakobo 3:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Lilime timaligwiritsa ntchito potamanda Yehova,* amene ndi Atate, komanso ndi lilime lomwelo timatemberera anthu amene analengedwa “mʼchifaniziro cha Mulungu.”+ 10 Pakamwa pamodzi pomwepo pamatuluka mawu otamanda komanso otemberera.
Abale anga, nʼzosayenera kuti zinthu zizichitika mwa njira imeneyi.+
-