Ekisodo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukapeza ngʼombe kapena bulu wa mdani wanu atasochera, muzimubweza ndithu kwa mwiniwake.+ Mateyu 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ine ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kupempherera amene akukuzunzani,+ Luka 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma inu amene mukumvetseranu, ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu ndi kuchitira zabwino amene akudana nanu.+
27 Koma inu amene mukumvetseranu, ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu ndi kuchitira zabwino amene akudana nanu.+