Ekisodo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musalakelake nyumba ya mnzanu. Musalakelake mkazi wa mnzanu,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ngʼombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzanu.”+
17 Musalakelake nyumba ya mnzanu. Musalakelake mkazi wa mnzanu,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ngʼombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzanu.”+