Aefeso 5:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi zonse muzitsimikizira kuti chovomerezeka+ kwa Ambuye nʼchiti. 11 Ndipo musiye kuchita nawo ntchito zosapindulitsa zamumdima.+ Mʼmalomwake, muzisonyeza poyera kuti ndi zinthu zoipa.
10 Nthawi zonse muzitsimikizira kuti chovomerezeka+ kwa Ambuye nʼchiti. 11 Ndipo musiye kuchita nawo ntchito zosapindulitsa zamumdima.+ Mʼmalomwake, muzisonyeza poyera kuti ndi zinthu zoipa.