19 Kodi inu simukudziwa kuti thupi lanu ndi kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu, womwe munapatsidwa ndi Mulungu?+ Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+ 20 chifukwa munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+