2 Samueli 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Nʼchifukwa chake ndidzakuyamikani inu Yehova pakati pa mitundu ya anthu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ Salimo 18:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani, inu Yehova, pakati pa mitundu ya anthu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+
50 Nʼchifukwa chake ndidzakuyamikani inu Yehova pakati pa mitundu ya anthu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+
49 Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani, inu Yehova, pakati pa mitundu ya anthu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+