Agalatiya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo agawane zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+ Aheberi 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso musaiwale kuchita zabwino ndi kugawira ena zomwe muli nazo,+ chifukwa Mulungu amasangalala ndi nsembe zoterozo.+
6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo agawane zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+
16 Komanso musaiwale kuchita zabwino ndi kugawira ena zomwe muli nazo,+ chifukwa Mulungu amasangalala ndi nsembe zoterozo.+