18 Paulo atakhala kumeneko kwa masiku ndithu, anatsanzikana ndi abalewo ndipo anapitiriza ulendo wake wapamadzi kulowera ku Siriya. Pa ulendowu anapita limodzi ndi Purisila ndi Akula. Paulo anameta tsitsi lake ku Kenkereya+ chifukwa cha lonjezo limene anachita.