Machitidwe 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ wa ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisila, anali atangofika kumene kuchokera ku Italy, chifukwa Kalaudiyo anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kunyumba kwawo. Machitidwe 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ wa ku Alekizandiriya, amene ankalankhula mwaluso, anafika ku Efeso. Iyeyu ankadziwanso bwino Malemba. Machitidwe 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Ndiyeno Purisila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga nʼkumufotokozera njira ya Mulungu molondola. 2 Timoteyo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Undiperekere moni kwa Purisika ndi Akula+ komanso banja la Onesiforo.+
2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ wa ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisila, anali atangofika kumene kuchokera ku Italy, chifukwa Kalaudiyo anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kunyumba kwawo.
24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ wa ku Alekizandiriya, amene ankalankhula mwaluso, anafika ku Efeso. Iyeyu ankadziwanso bwino Malemba.
26 Munthu ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Ndiyeno Purisila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga nʼkumufotokozera njira ya Mulungu molondola.