Mateyu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chenjerani ndi aneneri abodza+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwa mitima yawo ali ngati mimbulu yolusa.+ Tito 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wolimbikitsa mpatuko,+ ukamudzudzula* koyamba ndi kachiwiri,+ usagwirizane nayenso+ 2 Yohane 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wina akabwera ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire mʼnyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.
15 Chenjerani ndi aneneri abodza+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwa mitima yawo ali ngati mimbulu yolusa.+
10 Wina akabwera ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire mʼnyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.