-
Aroma 4:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiye kodi anthu odulidwa okha ndi amene amakhala osangalala choncho? Kapena osadulidwa nawonso amakhala osangalala?+ Popeza timati: “Abulahamu anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake.”+ 10 Koma kodi iye anali wotani pamene anaonedwa kuti ndi wolungama? Kodi anali wodulidwa kapena wosadulidwa? Iyetu anali asanadulidwe.
-