Aroma 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa ku Chilamulo chimene chinkatimanga, kuti tikhale akapolo mʼnjira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati mʼnjira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+
6 Koma tsopano tamasulidwa ku Chilamulo,+ chifukwa tafa ku Chilamulo chimene chinkatimanga, kuti tikhale akapolo mʼnjira yatsopano motsogoleredwa ndi mzimu,+ osati mʼnjira yakale motsogoleredwa ndi malamulo olembedwa.+