Salimo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa palibe amene angakhulupirire chilichonse chimene anena.Mʼmitima yawo muli chidani chokhachokha.Mmero wawo ndi manda otseguka.Iwo amalankhula zachinyengo* ndi lilime lawo.+
9 Chifukwa palibe amene angakhulupirire chilichonse chimene anena.Mʼmitima yawo muli chidani chokhachokha.Mmero wawo ndi manda otseguka.Iwo amalankhula zachinyengo* ndi lilime lawo.+