-
Miyambo 5:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kasupe wako akhale wodalitsidwa,*
Ndipo uzisangalala ndi mkazi amene unamukwatira udakali wachinyamata.+
19 Iye akhale ngati mbawala yaikazi yachikondi komanso ngati kamwana ka mbuzi zamʼmapiri kokongola.+
Mabere ake azikukhutiritsa* nthawi zonse.
Chikondi chake chizikusangalatsa kwambiri nthawi zonse.+
-