Agalatiya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa kudulidwa kapena kusadulidwa nʼkosafunika,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+ Akolose 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero, sipadzakhala Mgiriki kapena Myuda, kudulidwa kapena kusadulidwa, mlendo, Msukuti,* kapolo kapena mfulu, chifukwa Khristu amachita zinthu zonse ndipo ife ndife ogwirizana naye.+
15 Chifukwa kudulidwa kapena kusadulidwa nʼkosafunika,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+
11 Mukatero, sipadzakhala Mgiriki kapena Myuda, kudulidwa kapena kusadulidwa, mlendo, Msukuti,* kapolo kapena mfulu, chifukwa Khristu amachita zinthu zonse ndipo ife ndife ogwirizana naye.+