2 Akorinto 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sitikuchita chilichonse chokhumudwitsa, kuti anthu asapezere chifukwa utumiki wathu.+ 2 Akorinto 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kapena kodi ndinalakwa pamene ndinadzichepetsa kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalalikira mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kulipira?+
7 Kapena kodi ndinalakwa pamene ndinadzichepetsa kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalalikira mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kulipira?+