Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona mʼchipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+ Numeri 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ine Yehova ndalankhula. Zimene ndidzachitire gulu lonse la anthu oipali, amene asonkhana kuti atsutsane ndi ine ndi izi: Onse adzafera mʼchipululu muno ndipo adzathera momwe muno.+
29 Mitembo yanu idzagona mʼchipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
35 Ine Yehova ndalankhula. Zimene ndidzachitire gulu lonse la anthu oipali, amene asonkhana kuti atsutsane ndi ine ndi izi: Onse adzafera mʼchipululu muno ndipo adzathera momwe muno.+