Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Akupitiriza kudya, Yesu anatenga mkate ndipo atayamika Mulungu, anaunyemanyema+ nʼkuupereka kwa ophunzira ake. Iye ananena kuti: “Eni, idyani. Mkate uwu ukuimira thupi langa.”+

  • Luka 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako anatenga mkate.+ Atayamika, anaunyemanyema nʼkuwapatsa ndipo anati: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu.+ Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+

  • 1 Akorinto 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma Mulungu anaika ziwalo zonse za thupi, chilichonse pamalo ake, mmene iye anafunira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena