2 Akorinto 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anaphedwa pamtengo chifukwa cha kufooka, koma ali ndi moyo chifukwa cha mphamvu ya Mulungu.+ Nʼzoona kuti ifenso ndife ofooka limodzi naye, koma tidzakhala naye limodzi+ chifukwa cha mphamvu ya Mulungu imene ikugwira ntchito mwa inu.+
4 Iye anaphedwa pamtengo chifukwa cha kufooka, koma ali ndi moyo chifukwa cha mphamvu ya Mulungu.+ Nʼzoona kuti ifenso ndife ofooka limodzi naye, koma tidzakhala naye limodzi+ chifukwa cha mphamvu ya Mulungu imene ikugwira ntchito mwa inu.+