Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake. 1 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chilichonse cholengedwa ndi Mulungu nʼchabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati munthu wayamika Mulungu pakudya,
24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake.
4 Chifukwa chilichonse cholengedwa ndi Mulungu nʼchabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati munthu wayamika Mulungu pakudya,