Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mofanana ndi zimenezi, nanunso muzionetsa kuwala kwanu pamaso pa anthu,+ kuti aone ntchito zanu zabwino+ nʼkulemekeza Atate wanu wakumwamba.+ Akolose 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chilichonse chimene mukuchita mʼmawu kapena mu ntchito, muzichita zonse mʼdzina la Ambuye Yesu, ndipo muziyamika Mulungu Atate kudzera mwa iye.+
16 Mofanana ndi zimenezi, nanunso muzionetsa kuwala kwanu pamaso pa anthu,+ kuti aone ntchito zanu zabwino+ nʼkulemekeza Atate wanu wakumwamba.+
17 Chilichonse chimene mukuchita mʼmawu kapena mu ntchito, muzichita zonse mʼdzina la Ambuye Yesu, ndipo muziyamika Mulungu Atate kudzera mwa iye.+