Afilipi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abale, nonsenu muyesetse kumanditsanzira+ ndipo muzionetsetsa amene akuchita zinthu mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani. 2 Atesalonika 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sikuti tinachita zimenezi chifukwa choti tilibe ulamuliro wokupemphani kuti mutithandize,+ koma tinkafuna kuti tikupatseni chitsanzo choti muzitsanzira.+
17 Abale, nonsenu muyesetse kumanditsanzira+ ndipo muzionetsetsa amene akuchita zinthu mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani.
9 Sikuti tinachita zimenezi chifukwa choti tilibe ulamuliro wokupemphani kuti mutithandize,+ koma tinkafuna kuti tikupatseni chitsanzo choti muzitsanzira.+