1 Akorinto 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kwa ife Mulungu alipo mmodzi yekha,+ amene ndi Atate.+ Zinthu zonse zinachokera kwa iye, ndipo ifeyo ndife ake.+ Palinso Ambuye mmodzi, Yesu Khristu, amene zinthu zonse zinakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo ifeyo kudzera mwa iyeyo.
6 Koma kwa ife Mulungu alipo mmodzi yekha,+ amene ndi Atate.+ Zinthu zonse zinachokera kwa iye, ndipo ifeyo ndife ake.+ Palinso Ambuye mmodzi, Yesu Khristu, amene zinthu zonse zinakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo ifeyo kudzera mwa iyeyo.