5 Pitirizani kudziyesa kuti muone ngati mukadali ndi chikhulupiriro. Pitirizani kudziyesa kuti mudziwe kuti ndinu munthu wotani.+ Kodi simukudziwa kuti ndinu ogwirizana ndi Yesu Khristu? Muyenera kudziwa zimenezi, kupatulapo ngati muli osavomerezeka.