Aheberi 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo mwaiwaliratu malangizo okudandaulirani ngati amene bambo amauza ana ake kuti: “Mwana wanga, usapeputse chilango* cha Yehova,* kapena kutaya mtima pamene iye akukudzudzula.
5 Ndipo mwaiwaliratu malangizo okudandaulirani ngati amene bambo amauza ana ake kuti: “Mwana wanga, usapeputse chilango* cha Yehova,* kapena kutaya mtima pamene iye akukudzudzula.