Agalatiya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye kodi amene amakupatsani mzimu ndi kuchita zinthu zamphamvu pakati panu,+ amachita zimenezi chifukwa chakuti inuyo mukuchita ntchito za chilamulo kapena chifukwa chakuti munakhulupirira uthenga wabwino umene munamva?
5 Ndiye kodi amene amakupatsani mzimu ndi kuchita zinthu zamphamvu pakati panu,+ amachita zimenezi chifukwa chakuti inuyo mukuchita ntchito za chilamulo kapena chifukwa chakuti munakhulupirira uthenga wabwino umene munamva?