Aroma 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chikondi chanu chisakhale chachiphamaso.+ Muzinyansidwa ndi zoipa+ nʼkumayesetsa kuchita zabwino.