Mateyu 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iye anamuyankha kuti: “‘Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse ndi maganizo anu onse.’+ Aroma 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi sichilimbikitsa munthu kuchitira mnzake zoipa,+ choncho chikondi chimathandiza munthu kuti akwaniritse lamulo.+
37 Iye anamuyankha kuti: “‘Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse ndi maganizo anu onse.’+
10 Chikondi sichilimbikitsa munthu kuchitira mnzake zoipa,+ choncho chikondi chimathandiza munthu kuti akwaniritse lamulo.+