1 Akorinto 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikanakondadi kuti nonsenu muzilankhula malilime,*+ koma ndikuona kuti ndi bwino kuti muzinenera.+ Kunena zoona, wonenera amaposa wolankhula malilime, kupatulapo ngati wamalilimeyo akumasulira kuti alimbikitse mpingo.
5 Ndikanakondadi kuti nonsenu muzilankhula malilime,*+ koma ndikuona kuti ndi bwino kuti muzinenera.+ Kunena zoona, wonenera amaposa wolankhula malilime, kupatulapo ngati wamalilimeyo akumasulira kuti alimbikitse mpingo.