Aroma 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu onse akudziwa kuti ndinu omvera ndipo ndikusangalala nanu chifukwa cha zimenezi. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru pa zinthu zabwino koma osadziwa kanthu pa zinthu zoipa.+
19 Anthu onse akudziwa kuti ndinu omvera ndipo ndikusangalala nanu chifukwa cha zimenezi. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru pa zinthu zabwino koma osadziwa kanthu pa zinthu zoipa.+