Machitidwe 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri ndi aphunzitsi.+ Iwo anali Baranaba, Sumiyoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo wa ku Kurene, Saulo ndiponso Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo.
13 Mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri ndi aphunzitsi.+ Iwo anali Baranaba, Sumiyoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo wa ku Kurene, Saulo ndiponso Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo.