Yona 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona moti Yona anakhala mʼmimba mwa nsomba masiku atatu, masana ndi usiku.+ Luka 24:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 ndipo anawauza kuti, “Malemba amanena kuti: Khristu adzazunzika ndipo tsiku lachitatu adzauka kwa akufa,+
17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona moti Yona anakhala mʼmimba mwa nsomba masiku atatu, masana ndi usiku.+
46 ndipo anawauza kuti, “Malemba amanena kuti: Khristu adzazunzika ndipo tsiku lachitatu adzauka kwa akufa,+