Mateyu 28:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ophunzira 11 aja anapita ku Galileya,+ kuphiri kumene Yesu anawauza kuti akakumane nawo.+ 17 Atamuona anamugwadira, koma ena anakayikira ngati analidi iyeyo.
16 Koma ophunzira 11 aja anapita ku Galileya,+ kuphiri kumene Yesu anawauza kuti akakumane nawo.+ 17 Atamuona anamugwadira, koma ena anakayikira ngati analidi iyeyo.