Yohane 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira ine, ngakhale atamwalira, adzakhalanso ndi moyo.
25 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira ine, ngakhale atamwalira, adzakhalanso ndi moyo.