Chivumbulutso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+
5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+