Genesis 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Mulungu anapanga zounikira ziwiri. Chounikira chowala kwambiri anachipanga kuti chiziwala* masana,+ ndipo chowala pangʼono kuti chiziwala* usiku, komanso anapanga nyenyezi.+
16 Choncho Mulungu anapanga zounikira ziwiri. Chounikira chowala kwambiri anachipanga kuti chiziwala* masana,+ ndipo chowala pangʼono kuti chiziwala* usiku, komanso anapanga nyenyezi.+