Hoseya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzawombola anthu anga ku mphamvu za Manda.*Ndidzawapulumutsa ku imfa.+ Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+ Iwe Manda, kodi mphamvu yako yowononga ili kuti?+ Koma Efuraimu sindimumvera chisoni.
14 Ine ndidzawombola anthu anga ku mphamvu za Manda.*Ndidzawapulumutsa ku imfa.+ Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+ Iwe Manda, kodi mphamvu yako yowononga ili kuti?+ Koma Efuraimu sindimumvera chisoni.