Machitidwe 19:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Izi zinachitika kwa zaka ziwiri, moti anthu onse okhala mʼchigawo cha Asia, Ayuda ndi Agiriki omwe, anamva mawu a Ambuye. 11 Mulungu anapitiriza kuchita zinthu zamphamvu komanso zodabwitsa kudzera mwa Paulo.+
10 Izi zinachitika kwa zaka ziwiri, moti anthu onse okhala mʼchigawo cha Asia, Ayuda ndi Agiriki omwe, anamva mawu a Ambuye. 11 Mulungu anapitiriza kuchita zinthu zamphamvu komanso zodabwitsa kudzera mwa Paulo.+