Aroma 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za thupi.+ Koma otsatira mzimu, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za mzimu.+
5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za thupi.+ Koma otsatira mzimu, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za mzimu.+