-
Aroma 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho Mulungu amene amatipatsa mphamvu kuti tithe kupirira ndiponso amene amatitonthoza, akuthandizeni nonsenu kukhala ndi maganizo amene Khristu Yesu anali nawo,
-