-
2 Akorinto 12:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndikuopa kuti ndikadzafika, mwina sindidzakupezani mmene ndikufunira ndipo mwina inenso sindidzakhala mmene mukufunira. Mʼmalomwake, nʼkutheka kuti padzakhala ndewu, nsanje, kukwiyitsana, mikangano, miseche, manongʼonongʼo, kudzitukumula ndiponso chipwirikiti.
-