1 Akorinto 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu asamadzinamize. Ngati aliyense wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.
18 Munthu asamadzinamize. Ngati aliyense wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.