-
Machitidwe 23:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Hananiya mkulu wa ansembe atamva zimenezi, analamula anthu amene anaimirira pafupi naye kuti amʼmenye pakamwa.
-